Mulandu Wa Chilima Watha Chifukwa Maumboni Ena Amaloza Munthu Wamkulu - Bon Kalindo

Описание к видео Mulandu Wa Chilima Watha Chifukwa Maumboni Ena Amaloza Munthu Wamkulu - Bon Kalindo

On Nyasa VoiceBox, discussions about why the vice president's corruption case was discontinued continue, with many Malawians speculating on the reasons behind it. As we await the Director of Public Prosecution to brief Parliament's Legal Affairs Committee on the matter as required by the constitution, Bon Kalindo suggests that the case couldn't have gone forward because the evidence pointed toward the President himself.

Pa Nyasa VoiceBox, zokambilana zokhuza chifukwa chomwe nkhani ya katangale wa wachiwiri kwa president idalekeka zikupitilira pomwe Amalawi ambiri akungoganizira zomwe zidapangitsa nkhaniyi. Pamene tikudikira mkulu wowona za milandu ku nyumba ya malamulo kuti adziwitse komiti yowona za malamulo ku Nyumba ya Malamulo pa nkhaniyi malinga ndi lamulo ladziko lino, a Bon Kalindo akuona kuti mlanduwu sukadapitira patsogolo chifukwa umboniwo unaloza kwa mtsogoleri wa dziko.

#malawi

Комментарии

Информация по комментариям в разработке